Yohane 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndinachokera kwa Atate ndipo ndinabwera m’dziko. Tsopano ndikuchoka m’dziko kupita kwa Atate.”+