Yohane 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tadziwa tsopano kuti inu mukudziwa zonse+ ndipo m’posafunikanso kuti munthu akufunseni mafunso.+ Pa chifukwa chimenechi tikukhulupirira kuti munachokeradi kwa Mulungu.”+
30 Tadziwa tsopano kuti inu mukudziwa zonse+ ndipo m’posafunikanso kuti munthu akufunseni mafunso.+ Pa chifukwa chimenechi tikukhulupirira kuti munachokeradi kwa Mulungu.”+