-
Yohane 21:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Anamufunsanso kachitatu: “Simoni mwana wa Yohane, kodi ine umandikonda kwambiri?” Petulo anamva chisoni kumva akumufunsa kachitatu kuti: “Kodi ine umandikonda kwambiri?” Choncho iye anati: “Ambuye, inu mumadziwa zonse,+ mukudziwanso bwino kuti ndimakukondani kwambiri.” Yesu anati: “Dyetsa ana a nkhosa anga.+
-