Maliko 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma nthawi yomweyo Yesu anazindikira mumtima mwake kuti iwo anali kuganiza zimenezo, ndipo anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zimenezi m’mitima mwanu?+ Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Yesu sanawakhulupirire+ kwenikweni chifukwa onsewo anali kuwadziwa. Yohane 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso, iye sanafunikire wina woti achite kumuuza za munthu, chifukwa payekha anali kudziwa zimene zili m’mitima ya anthu.+ Yohane 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tadziwa tsopano kuti inu mukudziwa zonse+ ndipo m’posafunikanso kuti munthu akufunseni mafunso.+ Pa chifukwa chimenechi tikukhulupirira kuti munachokeradi kwa Mulungu.”+
8 Koma nthawi yomweyo Yesu anazindikira mumtima mwake kuti iwo anali kuganiza zimenezo, ndipo anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zimenezi m’mitima mwanu?+
25 Komanso, iye sanafunikire wina woti achite kumuuza za munthu, chifukwa payekha anali kudziwa zimene zili m’mitima ya anthu.+
30 Tadziwa tsopano kuti inu mukudziwa zonse+ ndipo m’posafunikanso kuti munthu akufunseni mafunso.+ Pa chifukwa chimenechi tikukhulupirira kuti munachokeradi kwa Mulungu.”+