Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+

      Ndipo khazikitsani wolungama.+

      Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+

  • Mateyu 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma Yesu, podziwa zimene iwo anali kuganiza,+ ananena kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zinthu zoipa m’mitima mwanu?+

  • Luka 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma iye anadziwa zimene iwo anali kuganiza.+ Choncho anauza munthu wa dzanja lopuwalayo kuti: “Nyamuka, uimirire pakatipa.” Munthuyo ananyamuka n’kuima chilili.+

  • Aheberi 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+

  • Chivumbulutso 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ana ake ndidzawapha ndi mliri wakupha, moti mipingo yonse idzadziwa kuti ineyo ndiye amene ndimafufuza impso ndi mitima, ndipo ndidzabwezera mmodzi ndi mmodzi wa inu malinga ndi ntchito zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena