Yohane 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ayudawo anamuyankha kuti: “Tili ndi chilamulo ife,+ ndipo malinga ndi chilamulocho iyeyu ayenera kufa, chifukwa akudziyesa mwana wa Mulungu.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 296 Nsanja ya Olonda,6/1/2008, tsa. 271/15/1991, tsa. 8
7 Ayudawo anamuyankha kuti: “Tili ndi chilamulo ife,+ ndipo malinga ndi chilamulocho iyeyu ayenera kufa, chifukwa akudziyesa mwana wa Mulungu.”+