Yohane 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ili linali tsiku lokonzekera+ pasika, ndipo nthawi inali cha m’ma 12 koloko masana.* Pamenepo iye anauza Ayudawo kuti: “Taonani! Mfumu yanu imeneyi!” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:14 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, tsa. 21
14 Ili linali tsiku lokonzekera+ pasika, ndipo nthawi inali cha m’ma 12 koloko masana.* Pamenepo iye anauza Ayudawo kuti: “Taonani! Mfumu yanu imeneyi!”