Yohane 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapafupi ndi mtengo wozunzikirapo wa Yesu, panaimirira mayi ake+ ndi m’bale wa mayi akewo, Mariya+ mkazi wa Kulopa, ndi Mariya Mmagadala.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:25 Yesu—Ndi Njira, tsa. 300 Nsanja ya Olonda,9/1/2010, tsa. 15
25 Koma chapafupi ndi mtengo wozunzikirapo wa Yesu, panaimirira mayi ake+ ndi m’bale wa mayi akewo, Mariya+ mkazi wa Kulopa, ndi Mariya Mmagadala.+