Yohane 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu amene anaona zimenezo akuchitira umboni, ndipo umboni wakewo ndi woona. Munthu ameneyu akudziwa kuti amanena zoona, kuti inunso mukhulupirire.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:35 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 15
35 Munthu amene anaona zimenezo akuchitira umboni, ndipo umboni wakewo ndi woona. Munthu ameneyu akudziwa kuti amanena zoona, kuti inunso mukhulupirire.+