Machitidwe 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma chiwembu chawocho chinadziwika kwa Saulo. Komabe iwo anali kuyang’anira mosamala m’zipata zonse usana ndi usiku kuti amuphe.+
24 Koma chiwembu chawocho chinadziwika kwa Saulo. Komabe iwo anali kuyang’anira mosamala m’zipata zonse usana ndi usiku kuti amuphe.+