Machitidwe 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma anamva njala kwambiri ndipo anafuna kudya. Pamene chakudya chinali kukonzedwa, anayamba kuona masomphenya.+
10 Koma anamva njala kwambiri ndipo anafuna kudya. Pamene chakudya chinali kukonzedwa, anayamba kuona masomphenya.+