-
Machitidwe 11:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Ndinali kupemphera mumzinda wa Yopa. Ndipo ndinayamba kuona masomphenya. M’masomphenyawo ndinaona chinthu chikutsika. Chinthucho chinali chooneka ngati chinsalu chachikulu chimene achigwira m’makona onse anayi, ndipo anali kuchitsitsa kuchokera kumwamba moti chinafika kwa ine.
-