Machitidwe 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero ndi manja awo analemba kuti: “Ife abale anu atumwi pamodzi ndi akulu, tikulembera inu abale athu ochokera mwa anthu a mitundu ina, okhala ku Antiokeya,+ ku Siriya ndi ku Kilikiya:+ Landirani moni! Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:23 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 26
23 Chotero ndi manja awo analemba kuti: “Ife abale anu atumwi pamodzi ndi akulu, tikulembera inu abale athu ochokera mwa anthu a mitundu ina, okhala ku Antiokeya,+ ku Siriya ndi ku Kilikiya:+ Landirani moni!