Machitidwe 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno analemba kalata nʼkuwapatsira yonena kuti: “Ife abale anu atumwi pamodzi ndi akulu, tikulembera inu abale athu ochokera mʼmitundu ina, amene muli ku Antiokeya,+ ku Siriya ndi ku Kilikiya: Landirani moni! Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:23 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 26
23 Ndiyeno analemba kalata nʼkuwapatsira yonena kuti: “Ife abale anu atumwi pamodzi ndi akulu, tikulembera inu abale athu ochokera mʼmitundu ina, amene muli ku Antiokeya,+ ku Siriya ndi ku Kilikiya: Landirani moni!