Machitidwe 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:15 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 132 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 329/15/1996, ptsa. 27-28 Mphunzitsi Waluso, tsa. 95
15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+
16:15 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 132 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 329/15/1996, ptsa. 27-28 Mphunzitsi Waluso, tsa. 95