Machitidwe 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anakhala akuchita zimenezi kwa masiku ambiri. Potsirizira pake Paulo anatopa nazo+ ndipo anatembenuka n’kuuza mzimuwo kuti: “Ndikukulamula m’dzina la Yesu Khristu kuti utuluke mwa mtsikanayu.”+ Nthawi yomweyo mzimuwo unatuluka.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:18 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, tsa. 74/1/1994, tsa. 316/15/1990, tsa. 16
18 Iye anakhala akuchita zimenezi kwa masiku ambiri. Potsirizira pake Paulo anatopa nazo+ ndipo anatembenuka n’kuuza mzimuwo kuti: “Ndikukulamula m’dzina la Yesu Khristu kuti utuluke mwa mtsikanayu.”+ Nthawi yomweyo mzimuwo unatuluka.+