Machitidwe 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinali kukhalira nanu nthawi zonse kuchokera tsiku loyamba limene ndinaponda m’chigawo cha Asia.+
18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinali kukhalira nanu nthawi zonse kuchokera tsiku loyamba limene ndinaponda m’chigawo cha Asia.+