Machitidwe 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Teritulo atapatsidwa mwayi kuti alankhulepo, anayamba kuneneza Paulo. Iye anati: “Tili pa mtendere wochuluka+ chifukwa cha inu, komanso zinthu zikusintha mu mtundu wathuwu chifukwa cha nzeru zanu zoona patali. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:2 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 192
2 Teritulo atapatsidwa mwayi kuti alankhulepo, anayamba kuneneza Paulo. Iye anati: “Tili pa mtendere wochuluka+ chifukwa cha inu, komanso zinthu zikusintha mu mtundu wathuwu chifukwa cha nzeru zanu zoona patali.