Machitidwe 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene bwanamkubwayo anagwedezera Paulo mutu kuti alankhule, Paulo anayankha kuti: “Ine podziwa bwino kuti mwakhala woweruza wa mtundu uwu kwa zaka zambiri, ndine wokondwa kuti ndilankhule podziteteza+ pa zimene akundinenezazi.
10 Pamene bwanamkubwayo anagwedezera Paulo mutu kuti alankhule, Paulo anayankha kuti: “Ine podziwa bwino kuti mwakhala woweruza wa mtundu uwu kwa zaka zambiri, ndine wokondwa kuti ndilankhule podziteteza+ pa zimene akundinenezazi.