Machitidwe 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngakhalenso panopa sangathe kukupatsani umboni+ wa zimene akundinenezazi.