Aroma 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anateronso kwa anthu amene anasinthanitsa choonadi+ cha Mulungu ndi bodza+ polambira chilengedwe ndi kuchichitira utumiki wopatulika m’malo mochita zimenezo kwa Iye amene anazilenga, amene ndi wotamandika kosatha. Ame. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:25 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13 Nsanja ya Olonda,6/15/1993, ptsa. 12-13
25 Anateronso kwa anthu amene anasinthanitsa choonadi+ cha Mulungu ndi bodza+ polambira chilengedwe ndi kuchichitira utumiki wopatulika m’malo mochita zimenezo kwa Iye amene anazilenga, amene ndi wotamandika kosatha. Ame.