Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Chifukwa cha kutukumuka mtima kwake, woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.+

      Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+

  • Salimo 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:

      “Kulibe Yehova.”+

      Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.

      Palibe amene akuchita zabwino.+

  • Malaki 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Inu mwanena kuti, ‘Kutumikira Mulungu n’kopanda phindu.+ Tapindulanji chifukwa chomutumikira ndiponso chifukwa choyenda mwachisoni pamaso pa Yehova wa makamu?+

  • Yohane 8:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Inu ndinu ochokera kwa atate wanu Mdyerekezi,+ ndipo mukufuna kuchita zokhumba za atate wanu.+ Iyeyo ndi wopha anthu chiyambire kupanduka kwake,+ ndipo sanakhazikike m’choonadi, chifukwa mwa iye mulibe choonadi. Pamene akunena bodza, amalankhula za m’mutu mwake, chifukwa iye ndi wabodza komanso tate wake wa bodza.+

  • 2 Atesalonika 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+

  • 2 Timoteyo 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi, n’kutembenukira ku nkhani zonama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena