Mateyu 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mzimu unatsogolera Yesu kuchipululu+ kuti akayesedwe+ ndi Mdyerekezi. Mateyu 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo. 1 Petulo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+ Chivumbulutso 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.
39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo.
8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+
9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.