Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 21:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kodi Wamphamvuyonse ndani kuti tim’tumikire?+

      Ndipo kulankhula naye kungatipindulitse chiyani?’+

  • Salimo 73:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndithudi, ndayeretsa mtima wanga pachabe,+

      Ndipo ndasamba m’manja mwanga pachabe posonyeza kuti ndine wopanda cholakwa.+

  • Yesaya 58:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano iwo akunena kuti: “‘Kodi ifeyo tinavutikiranji kusala kudya inu osaona,+ ndipo tinadzisautsiranji+ inu osasamala n’komwe?’+

      “Komatu anthu inu munali kusangalala tsiku limene munali kusala kudya, pamene antchito anu onse munali kuwagwiritsa ntchito yakalavulagaga.+

  • Zefaniya 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Pa nthawi imeneyo ndidzafufuza ndi nyale mu Yerusalemu mosamala kwambiri,+ ndipo ndidzalanga anthu amene akukhala mosatekeseka ngati vinyo amene nsenga zake zakhazikika pansi.+ M’mitima yawo, anthu amenewa akunena kuti, ‘Yehova sadzachita zabwino kapena kuchita zoipa.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena