Levitiko 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “M’mwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo,+ muzidzisautsa*+ ndipo aliyense wa inu asamagwire ntchito ina iliyonse,+ kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu. Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale.+ Salimo 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+
29 “M’mwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo,+ muzidzisautsa*+ ndipo aliyense wa inu asamagwire ntchito ina iliyonse,+ kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu. Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale.+
13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+