Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Mika 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa nthawiyo adzafuulira Yehova kuti awathandize, koma sadzawayankha.+ Adzawabisira nkhope yake pa nthawi imeneyo+ chifukwa cha zoipa zimene anali kuchita.+
4 Pa nthawiyo adzafuulira Yehova kuti awathandize, koma sadzawayankha.+ Adzawabisira nkhope yake pa nthawi imeneyo+ chifukwa cha zoipa zimene anali kuchita.+