Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 31:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo mkwiyo wanga udzawayakira tsiku limenelo,+ ndipo ndidzawasiya+ ndi kuwabisira nkhope yanga,+ motero adzakhala chinthu choyenera kuwonongedwa. Masoka ndi zowawa zambiri zidzawagwera,+ ndipo pa tsiku limenelo adzanena kuti, ‘Masoka amenewatu akutigwera chifukwa chakuti Mulungu wathu sali pakati pathu.’+

  • Yeremiya 33:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Wanenanso mawu okhudza amuna amene akubwera kudzamenyana ndi Akasidi, ndiponso okhudza malo amene adzaza ndi mitembo ya amuna amene wawapha chifukwa cha mkwiyo wake waukulu,+ amenenso ali oipa kwambiri moti iye wausiya mzindawu chifukwa cha kuipa kwa anthu amenewo.+

  • Maliro 3:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Mwadzitchinga ndi mtambo waukulu+ kuti pemphero lisadutse ndi kufika kwa inu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena