Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 80:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Inu Yehova Mulungu wa makamu, mudzakwiyira mapemphero a anthu anu mpaka liti?+

  • Miyambo 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+

  • Miyambo 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Munthu amene amathawitsa khutu lake kuti asamve chilamulo,+ ngakhale pemphero lake limakhala lonyansa.+

  • Yesaya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+

  • Yeremiya 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova anapitiriza kundiuza kuti: “Usapempherere anthu awa kuti zinthu ziwayendere bwino.+

  • Mika 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pa nthawiyo adzafuulira Yehova kuti awathandize, koma sadzawayankha.+ Adzawabisira nkhope yake pa nthawi imeneyo+ chifukwa cha zoipa zimene anali kuchita.+

  • Zekariya 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “‘Popeza kuti ine ndikawaitana sanali kundimvera,+ iwonso akandiitana sindinali kuwamvera,’+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena