Salimo 66:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndikuganizira choipa chilichonse mumtima mwanga,Yehova sadzandimvera.+ Salimo 109:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene akuweruzidwa amuweruze kuti ndi woipa.Ndipo pemphero lake likhale tchimo.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+