Yobu 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi Mulungu angamumvere kulira kwakeZowawa zikamugwera?+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Miyambo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene amathawitsa khutu lake kuti asamve chilamulo,+ ngakhale pemphero lake limakhala lonyansa.+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+ Yohane 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu ali woopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, ameneyo amamumvetsera.+ Yakobo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumapempha koma simulandira, chifukwa mukupempha ndi cholinga choipa,+ kuti mukhutiritse zilakolako za matupi anu.+
9 Munthu amene amathawitsa khutu lake kuti asamve chilamulo,+ ngakhale pemphero lake limakhala lonyansa.+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+
31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu ali woopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, ameneyo amamumvetsera.+
3 Mumapempha koma simulandira, chifukwa mukupempha ndi cholinga choipa,+ kuti mukhutiritse zilakolako za matupi anu.+