Aroma 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kapena kodi ukunyoza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ kwake ndi kuleza mtima kwake,+ chifukwa chakuti sudziwa kuti cholinga cha kukoma mtima kwa Mulungu ndicho kukuthandiza kuti ulape?+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda,11/1/2001, tsa. 13
4 Kapena kodi ukunyoza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ kwake ndi kuleza mtima kwake,+ chifukwa chakuti sudziwa kuti cholinga cha kukoma mtima kwa Mulungu ndicho kukuthandiza kuti ulape?+