Aroma 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:28 Nsanja ya Olonda,2/1/1998, tsa. 16
28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+