Aroma 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ngati Mulungu alidi mmodzi.+ Iye ndi amene adzayese anthu odulidwa+ kuti ndi olungama chifukwa cha chikhulupiriro, ndiponso anthu osadulidwa+ adzawayesa olungama mwa chikhulupiriro chawo.
30 ngati Mulungu alidi mmodzi.+ Iye ndi amene adzayese anthu odulidwa+ kuti ndi olungama chifukwa cha chikhulupiriro, ndiponso anthu osadulidwa+ adzawayesa olungama mwa chikhulupiriro chawo.