Aroma 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma kodi Lemba limati chiyani? Limati: “Mawu a chilamulowo ali pafupi ndi iwe, ali m’kamwa mwako ndi mumtima mwako,”+ amenewa ndi “mawu”+ a chikhulupiriro, amene tikulalikira.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:8 Nsanja ya Olonda,12/15/1997, tsa. 19
8 Koma kodi Lemba limati chiyani? Limati: “Mawu a chilamulowo ali pafupi ndi iwe, ali m’kamwa mwako ndi mumtima mwako,”+ amenewa ndi “mawu”+ a chikhulupiriro, amene tikulalikira.+