-
Aroma 15:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndi zoona kuti achita zimenezo mwa kufuna kwawo, komabe iwo anali ndi ngongole kwa oyerawo. Pakuti ngati anthu a mitundu ina alandirako zinthu zauzimu+ kuchokera kwa oyerawo, ndiye kuti anthu a mitundu inawo ayeneranso kutumikira oyera amenewa mwa kuwapatsa zinthu zofunika pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku.+
-