1 Akorinto 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mukuona mmene anakuitanirani, abale, kuti si ambiri amene anthu amawaona kuti ndi anzeru+ omwe anaitanidwa,+ si ambiri amphamvu+ amene anaitanidwa, si ambiri a m’mabanja achifumu. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:26 Nsanja ya Olonda,8/15/1994, ptsa. 12-137/1/1988, ptsa. 28-29
26 Mukuona mmene anakuitanirani, abale, kuti si ambiri amene anthu amawaona kuti ndi anzeru+ omwe anaitanidwa,+ si ambiri amphamvu+ amene anaitanidwa, si ambiri a m’mabanja achifumu.