1 Akorinto 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti ufumu wa Mulungu sunagone m’mawu, koma mu mphamvu.+