1 Akorinto 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu waika ziwalo zosiyanasiyana mumpingo.+ Choyamba atumwi,+ chachiwiri aneneri,+ chachitatu aphunzitsi,+ kenako ntchito zamphamvu,+ mphatso za kuchiritsa,+ utumiki wothandiza anthu,+ luso loyendetsa zinthu,+ ndi malilime osiyanasiyana.+
28 Mulungu waika ziwalo zosiyanasiyana mumpingo.+ Choyamba atumwi,+ chachiwiri aneneri,+ chachitatu aphunzitsi,+ kenako ntchito zamphamvu,+ mphatso za kuchiritsa,+ utumiki wothandiza anthu,+ luso loyendetsa zinthu,+ ndi malilime osiyanasiyana.+