2 Akorinto 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti Mwana wa Mulungu,+ Khristu Yesu, amene analalikidwa pakati panu kudzera mwa ineyo, Silivano, ndi Timoteyo,+ sanakhale Inde kenako Ayi, koma mwa iye, Inde wakhalabe Inde.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,3/15/2014, tsa. 31
19 Pakuti Mwana wa Mulungu,+ Khristu Yesu, amene analalikidwa pakati panu kudzera mwa ineyo, Silivano, ndi Timoteyo,+ sanakhale Inde kenako Ayi, koma mwa iye, Inde wakhalabe Inde.+