2 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ngati ogwidwa ndi chisoni koma osangalala nthawi zonse, ngati osauka koma olemeretsa anthu ambiri, ngati opanda kalikonse koma okhala ndi zinthu zonse.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:10 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 20
10 ngati ogwidwa ndi chisoni koma osangalala nthawi zonse, ngati osauka koma olemeretsa anthu ambiri, ngati opanda kalikonse koma okhala ndi zinthu zonse.+