Aefeso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 290
2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+