Aefeso 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa chifukwa chimenechi, inuyo mukawerenga zimenezi mutha kuzindikira kuti chinsinsi chopatulika+ chonena za Khristu ndikuchimvetsa bwino.+
4 Pa chifukwa chimenechi, inuyo mukawerenga zimenezi mutha kuzindikira kuti chinsinsi chopatulika+ chonena za Khristu ndikuchimvetsa bwino.+