Aefeso 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mibadwo ina, chinsinsi+ chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene chaululidwira+ tsopano kwa atumwi ndi aneneri+ ake oyera mwa mzimu. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,2/15/2006, tsa. 19
5 M’mibadwo ina, chinsinsi+ chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene chaululidwira+ tsopano kwa atumwi ndi aneneri+ ake oyera mwa mzimu.