Aefeso 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muziyenda modzichepetsa nthawi zonse,+ mofatsa, moleza mtima,+ ndiponso mololerana m’chikondi.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2016, tsa. 22 Nsanja ya Olonda,7/15/2012, tsa. 28