Afilipi 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Si kuti ndikulankhula izi kusonyeza kuti ndikusowa kanthu, pakuti m’zochitika zosiyanasiyana ine ndaphunzira kukhala wokhutira ndi zimene ndili nazo.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Nsanja ya Olonda,6/1/2003, ptsa. 8-11
11 Si kuti ndikulankhula izi kusonyeza kuti ndikusowa kanthu, pakuti m’zochitika zosiyanasiyana ine ndaphunzira kukhala wokhutira ndi zimene ndili nazo.+