Afilipi 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Sindikulankhula zimenezi chifukwa chakuti ndikusowa kanthu, chifukwa ndaphunzira kukhala wokhutira ndi zimene ndili nazo posatengera mmene zinthu zilili pa moyo wanga.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Nsanja ya Olonda,6/1/2003, ptsa. 8-11
11 Sindikulankhula zimenezi chifukwa chakuti ndikusowa kanthu, chifukwa ndaphunzira kukhala wokhutira ndi zimene ndili nazo posatengera mmene zinthu zilili pa moyo wanga.+