Afilipi 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Si kuti mtima wanga uli pa mphatsoyo ayi,+ koma ndikufunitsitsa kuti mulandire madalitso+ amene adzawonjezere phindu pa zimene muli nazo.
17 Si kuti mtima wanga uli pa mphatsoyo ayi,+ koma ndikufunitsitsa kuti mulandire madalitso+ amene adzawonjezere phindu pa zimene muli nazo.