1 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri, 1 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Utumiki wa Ufumu,2/2000, ptsa. 3-4
6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri,