1 Atesalonika 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti ngati timakhulupirira kuti Yesu anafa ndi kuukanso,+ ndiye kuti amenenso agona mu imfa kudzera mwa Yesu, Mulungu adzawasonkhanitsa kuti akhale naye limodzi.+
14 Pakuti ngati timakhulupirira kuti Yesu anafa ndi kuukanso,+ ndiye kuti amenenso agona mu imfa kudzera mwa Yesu, Mulungu adzawasonkhanitsa kuti akhale naye limodzi.+