1 Atesalonika 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti tikukuuzani izi mogwirizana ndi mawu a Yehova+ kuti, ife amoyofe amene tidzakhalapo pa nthawi ya kukhalapo* kwa Ambuye,+ sitidzakhala patsogolo pa amene agona mu imfa. 1 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Nsanja ya Olonda,1/1/2007, tsa. 281/15/1993, tsa. 5 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 103-104
15 Pakuti tikukuuzani izi mogwirizana ndi mawu a Yehova+ kuti, ife amoyofe amene tidzakhalapo pa nthawi ya kukhalapo* kwa Ambuye,+ sitidzakhala patsogolo pa amene agona mu imfa.